Deuteronomo 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo kapena mlandu wa mwana wamasiye,+ ndipo musamalande chovala cha mkazi wamasiye kuti chikhale chikole.+ Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+
17 Musamapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo kapena mlandu wa mwana wamasiye,+ ndipo musamalande chovala cha mkazi wamasiye kuti chikhale chikole.+
17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+
27 Kulambira* koyera komanso kosadetsedwa kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ amene akukumana ndi mavuto*+ komanso kupewa kuti dzikoli likuchititseni kukhala ndi banga.+