Mateyu 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu aliyense akamva mawu a Ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera nʼkuchotsa zimene zafesedwa mumtima wa munthuyo. Iyi ndi mbewu imene inafesedwa mʼmbali mwa msewu ija.+ Luka 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Mdyerekezi anamuuza kuti: “Ndikupatsani ulamuliro pa maufumu onsewa ndi ulemerero wawo wonse, chifukwa unaperekedwa kwa ine+ ndipo ndikhoza kuupereka kwa aliyense amene ndingakonde kumupatsa. Yohane 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano dziko ili likuweruzidwa, wolamulira wa dzikoli+ aponyedwa kunja tsopano.+
19 Munthu aliyense akamva mawu a Ufumu koma osazindikira tanthauzo lake, woipayo+ amabwera nʼkuchotsa zimene zafesedwa mumtima wa munthuyo. Iyi ndi mbewu imene inafesedwa mʼmbali mwa msewu ija.+
6 Ndiyeno Mdyerekezi anamuuza kuti: “Ndikupatsani ulamuliro pa maufumu onsewa ndi ulemerero wawo wonse, chifukwa unaperekedwa kwa ine+ ndipo ndikhoza kuupereka kwa aliyense amene ndingakonde kumupatsa.