Machitidwe 20:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu yopondereza idzafika pakati panu+ ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+
29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu yopondereza idzafika pakati panu+ ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi. 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+