Maliko 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona Simoni ndi Andireya+ mchimwene wake wa Simoniyo, akuponya maukonde awo mʼnyanjamo+ chifukwa anali asodzi.+ Yohane 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Andireya,+ mchimwene wake wa Simoni Petulo anali mmodzi wa awiriwo, amene anamva zimene Yohane ananena nʼkutsatira Yesu.
16 Pamene ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona Simoni ndi Andireya+ mchimwene wake wa Simoniyo, akuponya maukonde awo mʼnyanjamo+ chifukwa anali asodzi.+
40 Andireya,+ mchimwene wake wa Simoni Petulo anali mmodzi wa awiriwo, amene anamva zimene Yohane ananena nʼkutsatira Yesu.