Mateyu 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba mʼnyanja. Iwo anali asodzi ndipo mayina awo anali Simoni wotchedwa Petulo+ ndi Andireya.+
18 Pamene ankayenda mʼmbali mwa nyanja ya Galileya,* Yesu anaona amuna awiri apachibale akuponya ukonde wophera nsomba mʼnyanja. Iwo anali asodzi ndipo mayina awo anali Simoni wotchedwa Petulo+ ndi Andireya.+