Maliko 6:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso anawalamula kuti asatenge kanthu pa ulendowo koma ndodo yokha basi. Anawalamula kuti asatenge mkate, thumba la chakudya kapena ndalama* mʼzikwama zawo,+ 9 koma kuti avale nsapato ndiponso kuti asavale malaya awiri.*
8 Komanso anawalamula kuti asatenge kanthu pa ulendowo koma ndodo yokha basi. Anawalamula kuti asatenge mkate, thumba la chakudya kapena ndalama* mʼzikwama zawo,+ 9 koma kuti avale nsapato ndiponso kuti asavale malaya awiri.*