Mateyu 10:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musatenge golide, siliva kapena kopa* mʼzikwama zanu za ndalama.+ 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo kapena malaya awiri* kapena nsapato kapenanso ndodo+ chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+
9 Musatenge golide, siliva kapena kopa* mʼzikwama zanu za ndalama.+ 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo kapena malaya awiri* kapena nsapato kapenanso ndodo+ chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+