Machitidwe 5:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo anamvera malangizo akewa ndipo anaitanitsa atumwiwo. Ndiyeno anangowakwapula*+ nʼkuwalamula kuti asiye kulankhula mʼdzina la Yesu, kenako anawamasula. 2 Akorinto 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Maulendo 5 Ayuda anandikwapula zikwapu 40, kuchotsera chimodzi.+
40 Iwo anamvera malangizo akewa ndipo anaitanitsa atumwiwo. Ndiyeno anangowakwapula*+ nʼkuwalamula kuti asiye kulankhula mʼdzina la Yesu, kenako anawamasula.