Mateyu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chenjerani ndi anthu, chifukwa adzakutengerani kumakhoti aangʼono,+ ndipo adzakukwapulani+ mumasunagoge awo.+ Maliko 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma inu khalani ochenjera. Anthu adzakutengerani kumakhoti aangʼono+ ndipo adzakukwapulani mumasunagoge+ nʼkukuimikani pamaso pa abwanamkubwa ndi mafumu chifukwa ndinu otsatira anga, kuti iwowo aphunzire za ine.+
17 Chenjerani ndi anthu, chifukwa adzakutengerani kumakhoti aangʼono,+ ndipo adzakukwapulani+ mumasunagoge awo.+
9 Koma inu khalani ochenjera. Anthu adzakutengerani kumakhoti aangʼono+ ndipo adzakukwapulani mumasunagoge+ nʼkukuimikani pamaso pa abwanamkubwa ndi mafumu chifukwa ndinu otsatira anga, kuti iwowo aphunzire za ine.+