Mateyu 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atatero, anayendayenda mʼGalileya+ yense ndipo ankaphunzitsa mʼmasunagoge+ mwawo, ankalalikira uthenga wabwino wa Ufumu komanso ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+
23 Atatero, anayendayenda mʼGalileya+ yense ndipo ankaphunzitsa mʼmasunagoge+ mwawo, ankalalikira uthenga wabwino wa Ufumu komanso ankachiritsa matenda amtundu uliwonse amene anthu ankadwala.+