Luka 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako anapita ku Kaperenao, mzinda wa ku Galileya. Ndipo ankawaphunzitsa pa tsiku la Sabata.+