Maliko 1:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Onsewo anachoka nʼkupita ku Kaperenao. Sabata litangoyamba, anakalowa musunagoge nʼkuyamba kuphunzitsa.+ 22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake, chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati ngati alembi.+
21 Onsewo anachoka nʼkupita ku Kaperenao. Sabata litangoyamba, anakalowa musunagoge nʼkuyamba kuphunzitsa.+ 22 Mmenemo anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake, chifukwa ankawaphunzitsa monga munthu wokhala ndi ulamuliro, osati ngati alembi.+