Luka 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo aliyense amene wanena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma aliyense amene wanyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa.+ Aheberi 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati tikuchita machimo mwadala pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibenso nsembe ina imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+
10 Ndipo aliyense amene wanena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma aliyense amene wanyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa.+
26 Ngati tikuchita machimo mwadala pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibenso nsembe ina imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+