-
Mateyu 12:31, 32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Pa chifukwa chimenechi ndikukuuzani kuti, anthu adzakhululukidwa tchimo la mtundu uliwonse ndi mawu aliwonse onyoza, koma wonyoza mzimu sadzakhululukidwa.+ 32 Mwachitsanzo, aliyense wolankhula mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa.+ Koma aliyense wolankhula mawu onyoza mzimu woyera, sadzakhululukidwa, mʼnthawi* ino kapena ikubwerayo.+
-