Mateyu 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chimene chimalowa mʼkamwa mwa munthu si chimene chimamuipitsa, koma chimene chimatuluka mʼkamwa mwake nʼchimene chimamuipitsa.”+
11 Chimene chimalowa mʼkamwa mwa munthu si chimene chimamuipitsa, koma chimene chimatuluka mʼkamwa mwake nʼchimene chimamuipitsa.”+