Maliko 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Palibe chilichonse chochokera kunja kwa munthu nʼkulowa mʼthupi mwake chimene chingaipitse munthu. Koma zinthu zimene zimatuluka mwa munthu ndi zimene zimaipitsa munthu.”+ Aefeso 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mawu owola asamatuluke pakamwa panu,+ koma pazituluka mawu abwino okha kuti alimbikitse ena pakafunika kutero, kuti athandize anthu amene akumvetsera.+ Yakobo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilimenso ndi moto.+ Pa ziwalo zonse za thupi lathu, lilime ndi lodzaza ndi zinthu zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse+ komanso limayatsa moyo wonse wa munthu* ndipo lili ndi moto wa Gehena.*
15 Palibe chilichonse chochokera kunja kwa munthu nʼkulowa mʼthupi mwake chimene chingaipitse munthu. Koma zinthu zimene zimatuluka mwa munthu ndi zimene zimaipitsa munthu.”+
29 Mawu owola asamatuluke pakamwa panu,+ koma pazituluka mawu abwino okha kuti alimbikitse ena pakafunika kutero, kuti athandize anthu amene akumvetsera.+
6 Lilimenso ndi moto.+ Pa ziwalo zonse za thupi lathu, lilime ndi lodzaza ndi zinthu zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse+ komanso limayatsa moyo wonse wa munthu* ndipo lili ndi moto wa Gehena.*