Mlaliki 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa Mulungu woona adzaweruza chilichonse chimene anthu amachita kuphatikizapo chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati chili chabwino kapena choipa.+ Aroma 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho aliyense wa ife adzayankha yekha kwa Mulungu.+
14 Chifukwa Mulungu woona adzaweruza chilichonse chimene anthu amachita kuphatikizapo chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati chili chabwino kapena choipa.+