Mlaliki 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa Mulungu woona adzaweruza chilichonse chimene anthu amachita kuphatikizapo chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati chili chabwino kapena choipa.+ Mateyu 12:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu+ pa mawu aliwonse opanda pake amene iwo amalankhula. 2 Akorinto 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa aliyense wa ife adzaonekera kumpando woweruzira milandu wa Khristu, kuti alandire mphoto yake mogwirizana ndi zimene anachita ali mʼthupi, kaya zabwino kapena zoipa.+
14 Chifukwa Mulungu woona adzaweruza chilichonse chimene anthu amachita kuphatikizapo chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati chili chabwino kapena choipa.+
36 Ndikukuuzani kuti pa Tsiku la Chiweruzo, anthu adzayankha mlandu+ pa mawu aliwonse opanda pake amene iwo amalankhula.
10 Chifukwa aliyense wa ife adzaonekera kumpando woweruzira milandu wa Khristu, kuti alandire mphoto yake mogwirizana ndi zimene anachita ali mʼthupi, kaya zabwino kapena zoipa.+