Yohane 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Atate wanu Abulahamu ankasangalala kwambiri chifukwa ankayembekezera kuona tsiku langa, moti analionadi ndipo anasangalala.”+ Aefeso 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mʼmibadwo yamʼmbuyo, chinsinsi chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene Mulungu wachiululira panopa kwa atumwi ndi aneneri ake oyera kudzera mwa mzimu.+ 1 Petulo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aneneri amene analosera za kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu anakusonyezani, anafufuza za chipulumutso chimenechi mwakhama ndiponso mosamala kwambiri.+
56 Atate wanu Abulahamu ankasangalala kwambiri chifukwa ankayembekezera kuona tsiku langa, moti analionadi ndipo anasangalala.”+
5 Mʼmibadwo yamʼmbuyo, chinsinsi chimenechi sichinaululidwe kwa ana a anthu mmene Mulungu wachiululira panopa kwa atumwi ndi aneneri ake oyera kudzera mwa mzimu.+
10 Aneneri amene analosera za kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu anakusonyezani, anafufuza za chipulumutso chimenechi mwakhama ndiponso mosamala kwambiri.+