Mateyu 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa ndithu ndikukuuzani, aneneri ambiri komanso anthu olungama ankalakalaka kuti aone zinthu zimene mukuziona inuzi koma sanazione,+ komanso kuti amve zimene mukumva inuzi koma sanazimve.
17 Chifukwa ndithu ndikukuuzani, aneneri ambiri komanso anthu olungama ankalakalaka kuti aone zinthu zimene mukuziona inuzi koma sanazione,+ komanso kuti amve zimene mukumva inuzi koma sanazimve.