Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Tonsefe tikungoyendayenda uku ndi uku ngati nkhosa zosochera.+

      Aliyense akulowera njira yake

      Ndipo Yehova wachititsa kuti zolakwa za tonsefe zigwere pa ameneyo.+

  • Mateyu 10:5, 6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yesu anatumiza atumwi 12 amenewa ndipo anawapatsa malangizo awa:+ “Musapite mumsewu wa anthu a mitundu ina ndipo musalowe mumzinda uliwonse wa Asamariya.+ 6 Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipita kwa nkhosa zosochera za nyumba ya Isiraeli.+

  • Machitidwe 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mulungu atasankha Mtumiki wake, choyamba+ anamutumiza kwa inu, kuti adzakudalitseni pobweza aliyense wa inu kuti musiye ntchito zanu zoipa.”

  • Machitidwe 13:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Choncho Paulo ndi Baranaba analankhula molimba mtima kuti: “Inu munali oyenera kuti muyambe kuuzidwa mawu a Mulungu.+ Koma popeza mukuwakana ndipo mukudziweruza nokha kuti ndinu osayenera moyo wosatha, ife tikupita kwa anthu a mitundu ina.+

  • Aroma 15:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kunena zoona, Khristu anakhala mtumiki wa anthu odulidwa+ kuti atsimikizire kuti Mulungu ndi wokhulupirika posonyeza kuti malonjezo amene Mulunguyo anapatsa makolo awo ndi otsimikizirika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena