Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 15:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Kuopa Yehova nʼkumene kumaphunzitsa munthu kuchita zinthu mwanzeru,+

      Ndipo ulemerero umabwera pambuyo pa kudzichepetsa.+

  • Mateyu 20:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Sizikuyenera kukhala choncho pakati panu.+ Koma aliyense amene akufuna kuti akhale wamkulu pakati panu akuyenera kukhala mtumiki wanu+

  • Mateyu 23:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Aliyense amene amadzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense amene amadzichepetsa adzakwezedwa.+

  • Luka 9:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ndiyeno anawauza kuti: “Aliyense amene walandira mwana wamngʼono ngati uyu mʼdzina langa walandiranso ine. Ndipo aliyense amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+ Chifukwa aliyense amene amachita zinthu ngati mwana wamngʼono pakati panu ndi amene ali wamkulu.”+

  • Luka 14:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa aliyense amene amadzikweza adzatsitsidwa, koma aliyense amene amadzichepetsa adzakwezedwa.”+

  • Luka 22:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamngʼono+ kwambiri pa nonsenu, ndipo amene ali mtsogoleri akhale ngati wotumikira.

  • Yakobo 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Dzichepetseni pamaso pa Yehova*+ ndipo iye adzakukwezani.+

  • 1 Petulo 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chimodzimodzinso inu achinyamata, muzigonjera amuna achikulire.*+ Komanso nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa* chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu odzikuza. Koma anthu odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena