Mateyu 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mvetserani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ nʼkumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa nʼkumanga nsanja.+ Atatero anausiya mʼmanja mwa alimi nʼkupita kudziko lina.+
33 Mvetserani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ nʼkumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa nʼkumanga nsanja.+ Atatero anausiya mʼmanja mwa alimi nʼkupita kudziko lina.+