-
Machitidwe 13:45, 46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Ayuda ataona gulu la anthulo, anachita nsanje ndipo anayamba kutsutsa mwamwano zimene Paulo ankalankhula.+ 46 Choncho Paulo ndi Baranaba analankhula molimba mtima kuti: “Inu munali oyenera kuti muyambe kuuzidwa mawu a Mulungu.+ Koma popeza mukuwakana ndipo mukudziweruza nokha kuti ndinu osayenera moyo wosatha, ife tikupita kwa anthu a mitundu ina.+
-