Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako Elisa anayamba kupemphera kuti: “Inu Yehova, chonde mutseguleni maso kuti aone.”+ Nthawi yomweyo Yehova anatsegula maso a mtumikiyo, moti anaona kuti dera lonse lamapiri kuzungulira Elisa+ linadzaza ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo oyaka moto.+

  • Danieli 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mtsinje wa moto unkayenda kuchokera kwa iye.+ Panali atumiki okwana 1 miliyoni* amene ankatumikira nthawi zonse ndi atumiki enanso 100 miliyoni* amene ankatumikira pamaso pake nthawi zonse.+ Bwalo la milandu+ linayamba kuzenga mlandu ndipo mabuku anatsegulidwa.

  • Mateyu 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kenako Mdyerekezi uja anamusiya+ ndipo kunabwera angelo nʼkuyamba kumutumikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena