-
Yohane 18:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma Petulo anaima kunja pakhomo. Choncho wophunzira amene ankadziwana ndi mkulu wa ansembe uja, anapita kukalankhula ndi mlonda wapakhomo nʼkumulowetsa Petulo.
-