Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 27:39, 40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Anthu amene ankadutsa pafupi ankanena mawu onyoza Yesu+ ndipo ankapukusa+ mitu yawo 40 nʼkumanena kuti: “Iwe amene unkanena kuti ungathe kugwetsa kachisi nʼkumumanga mʼmasiku atatu,+ dzipulumutse! Ngati ulidi mwana wa Mulungu, tsikatu pamtengo wozunzikirapowo!”*+

  • Yohane 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Yesu anawayankha kuti: “Gwetsani kachisiyu ndipo ine ndidzamumanga mʼmasiku atatu.”+

  • Machitidwe 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mwachitsanzo, ife tamumva akunena kuti Yesu wa ku Nazareti uja adzawononga malo oyerawa nʼkusintha miyambo imene Mose anatipatsa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena