Maliko 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+ Luka 22:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Kenako kutacha, bungwe la akulu, kuphatikizapo ansembe aakulu komanso alembi, anasonkhana pamodzi,+ ndipo anamutengera kuholo ya Khoti Lalikulu la Ayuda.* Kumeneko iwo anati:
15 Mwamsanga mʼbandakucha, ansembe aakulu limodzi ndi akulu komanso alembi, kutanthauza Khoti lonse Lalikulu la Ayuda,* anasonkhana pamodzi kuti agwirizane zoti amuchite Yesu. Kenako anamumanga nʼkupita naye kukamupereka kwa Pilato.+
66 Kenako kutacha, bungwe la akulu, kuphatikizapo ansembe aakulu komanso alembi, anasonkhana pamodzi,+ ndipo anamutengera kuholo ya Khoti Lalikulu la Ayuda.* Kumeneko iwo anati: