Machitidwe 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Abale anga, zinali zofunika kuti lemba likwaniritsidwe, limene mzimu woyera unaneneratu kudzera mwa Davide. Lembali ndi lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Machitidwe 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 (Munthu ameneyu, anagula munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu nʼkuphulika mimba ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.+
16 “Abale anga, zinali zofunika kuti lemba likwaniritsidwe, limene mzimu woyera unaneneratu kudzera mwa Davide. Lembali ndi lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+
18 (Munthu ameneyu, anagula munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu nʼkuphulika mimba ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.+