Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 41:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Ngakhale munthu amene ndinkakhala naye mwamtendere, amene ndinkamukhulupirira,+

      Munthu amene ankadya chakudya changa, watukula chidendene chake nʼkundiukira.+

  • Salimo 55:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chifukwa amene akundinyoza si mdani.+

      Akanakhala mdani ndikanapirira.

      Amene wandiukira si munthu wodana nane kwambiri.

      Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.

  • Yohane 13:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha. Koma zimenezi zachitika kuti lemba likwaniritsidwe,+ limene limati: ‘Munthu amene ankadya chakudya changa, watukula chidendene chake nʼkundiukira.’*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena