Luka 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atamva zimenezi anamuumiriza mokweza mawu kuti Yesu aphedwe basi. Anthuwo ankafuula mwamphamvu moti Pilato anangololera.+ Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula.
23 Atamva zimenezi anamuumiriza mokweza mawu kuti Yesu aphedwe basi. Anthuwo ankafuula mwamphamvu moti Pilato anangololera.+
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula.