Maliko 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mawu osonyeza mlandu umene anamuphera anawalemba kuti: “Mfumu ya Ayuda.”+ Luka 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamwamba pake analembapo mawu akuti: “Uyu ndi Mfumu ya Ayuda.”+ Yohane 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pilato analembanso dzina laudindo nʼkuliika pamtengo wozunzikirapowo.* Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+
19 Pilato analembanso dzina laudindo nʼkuliika pamtengo wozunzikirapowo.* Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+