Luka 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu anangoima nʼkumaonerera zimene zinkachitikazo. Koma olamulira ankamunyogodola nʼkumanena kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, musiyeni adzipulumutse yekha, ngati alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+
35 Anthu anangoima nʼkumaonerera zimene zinkachitikazo. Koma olamulira ankamunyogodola nʼkumanena kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, musiyeni adzipulumutse yekha, ngati alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+