-
Mateyu 27:42, 43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika! Ngati ali Mfumu ya Isiraeli,+ tiyeni tione ngati angatsike pamtengo wozunzikirapowo* ndipo ife timukhulupirira. 43 Paja iye amakhulupirira Mulungu, ndiye panopa Mulunguyo amupulumutse ngati akumufunadi+ chifukwa iye ankanena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+
-