Luka 4:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yesu anabwerera ku Galileya+ atadzazidwa ndi mphamvu ya mzimu. Ndipo mbiri yake yabwino inamveka paliponse mʼmadera onse ozungulira. 15 Komanso anayamba kuphunzitsa mʼmasunagoge awo ndipo anthu onse ankamulemekeza. Luka 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pasanapite nthawi yaitali, Yesu anayamba kuyenda mumzinda ndi mzinda komanso mudzi ndi mudzi nʼkumalalikira komanso kulengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu.+ Ndipo atumwi 12 aja anali naye limodzi.
14 Tsopano Yesu anabwerera ku Galileya+ atadzazidwa ndi mphamvu ya mzimu. Ndipo mbiri yake yabwino inamveka paliponse mʼmadera onse ozungulira. 15 Komanso anayamba kuphunzitsa mʼmasunagoge awo ndipo anthu onse ankamulemekeza.
8 Pasanapite nthawi yaitali, Yesu anayamba kuyenda mumzinda ndi mzinda komanso mudzi ndi mudzi nʼkumalalikira komanso kulengeza uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu.+ Ndipo atumwi 12 aja anali naye limodzi.