Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kulikonse kumene munthu sakakulandirani kapena kumvetsera mawu anu, mukamatuluka mʼnyumba imeneyo kapena mumzinda umenewo muzisansa fumbi kumapazi anu.+

  • Luka 10:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mukalowa mumzinda umene sanakulandireni bwino, muzichokamo nʼkupita mʼmisewu yawo nʼkunena kuti: 11 ‘Tikukusansirani ngakhale fumbi lamumzinda wanu uno,+ limene lamatirira kumapazi kwathu. Komabe dziwani kuti Ufumu wa Mulungu wayandikira.’

  • Machitidwe 13:50, 51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Koma Ayuda anauza zoipa amayi otchuka oopa Mulungu komanso amuna olemekezeka amumzindawo. Choncho iwo anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo. 51 Koma Paulo ndi Baranaba anasansa fumbi kumapazi awo kuti ukhale umboni wowatsutsa nʼkupita ku Ikoniyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena