Levitiko 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usagone ndi mkazi wa mchimwene wako,+ chifukwa kumeneko nʼkuchititsa manyazi* mchimwene wako. Levitiko 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamuna akakwatira mkazi wa mchimwene wake, wachita chinthu chonyansa.+ Iye wachititsa manyazi* mchimwene wake. Mwamuna ndi mkaziyo ayenera kufa kuti asabereke ana.
21 Mwamuna akakwatira mkazi wa mchimwene wake, wachita chinthu chonyansa.+ Iye wachititsa manyazi* mchimwene wake. Mwamuna ndi mkaziyo ayenera kufa kuti asabereke ana.