Yohane 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu atakweza maso ake nʼkuona gulu lalikulu la anthu likubwera kwa iye, anafunsa Filipo kuti: “Kodi mitanda ya mkate yodyetsa anthu onsewa tingakaigule kuti?”+
5 Yesu atakweza maso ake nʼkuona gulu lalikulu la anthu likubwera kwa iye, anafunsa Filipo kuti: “Kodi mitanda ya mkate yodyetsa anthu onsewa tingakaigule kuti?”+