Mateyu 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chimene chimalowa mʼkamwa mwa munthu si chimene chimamuipitsa, koma chimene chimatuluka mʼkamwa mwake nʼchimene chimamuipitsa.”+ Tito 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zinthu zonse nʼzoyera kwa anthu oyera.+ Koma kwa anthu oipitsidwa ndi opanda chikhulupiriro kulibe choyera, chifukwa maganizo awo ndi chikumbumtima chawo nʼzoipitsidwa.+
11 Chimene chimalowa mʼkamwa mwa munthu si chimene chimamuipitsa, koma chimene chimatuluka mʼkamwa mwake nʼchimene chimamuipitsa.”+
15 Zinthu zonse nʼzoyera kwa anthu oyera.+ Koma kwa anthu oipitsidwa ndi opanda chikhulupiriro kulibe choyera, chifukwa maganizo awo ndi chikumbumtima chawo nʼzoipitsidwa.+