Mateyu 15:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anthu onsewo anadya nʼkukhuta, moti zotsala zimene anatolera zinadzaza madengu akuluakulu 7.+