Mateyu 12:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesu atadziwa zimenezi, anachoka pamalo amenewo. Anthu ambiri anamutsatira+ ndipo iye anawachiritsa onsewo, 16 koma anawalamula mwamphamvu kuti asamuulule.+ Maliko 8:29, 30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno anafunsa ophunzirawo kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti: “Ndinu Khristu.”+ 30 Atanena zimenezo, anawalamula mwamphamvu kuti asauze aliyense za iye.+
15 Yesu atadziwa zimenezi, anachoka pamalo amenewo. Anthu ambiri anamutsatira+ ndipo iye anawachiritsa onsewo, 16 koma anawalamula mwamphamvu kuti asamuulule.+
29 Ndiyeno anafunsa ophunzirawo kuti: “Nanga inuyo mumati ndine ndani?” Petulo anayankha kuti: “Ndinu Khristu.”+ 30 Atanena zimenezo, anawalamula mwamphamvu kuti asauze aliyense za iye.+