Mateyu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu ndinu mchere+ wa dziko lapansi. Koma ngati mchere watha mphamvu, kodi mphamvu yakeyo angaibwezeretse bwanji? Sungagwirenso ntchito iliyonse koma ungafunike kungoutaya kunja+ kuti anthu azikaupondaponda. Luka 14:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kunena zoona, mchere ndi wabwino. Koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvu yakeyo ingabwezeretsedwe bwanji?+ 35 Ndi wosayenera kuuthira munthaka kapena mʼmanyowa. Anthu amangoutaya kunja. Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+
13 Inu ndinu mchere+ wa dziko lapansi. Koma ngati mchere watha mphamvu, kodi mphamvu yakeyo angaibwezeretse bwanji? Sungagwirenso ntchito iliyonse koma ungafunike kungoutaya kunja+ kuti anthu azikaupondaponda.
34 Kunena zoona, mchere ndi wabwino. Koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvu yakeyo ingabwezeretsedwe bwanji?+ 35 Ndi wosayenera kuuthira munthaka kapena mʼmanyowa. Anthu amangoutaya kunja. Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+