Maliko 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mchere ndi wabwino, koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvuyo mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere mwa inu nokha+ ndipo sungani mtendere pakati panu.”+
50 Mchere ndi wabwino, koma ngati mcherewo watha mphamvu, kodi mphamvuyo mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere mwa inu nokha+ ndipo sungani mtendere pakati panu.”+