-
Machitidwe 4:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 dziwani nonsenu ndi Aisiraeli onse, kuti mʼdzina la Yesu Khristu wa ku Nazareti uja,+ amene inu munamuphera pamtengo,+ koma amene Mulungu anamuukitsa,+ kudzera mwa iyeyo munthuyu waima patsogolo panu ali bwinobwino. 11 Yesu ameneyu ndi ‘mwala umene inu omanga nyumba munauona ngati wopanda pake, umene tsopano wakhala mwala wofunika kwambiri wapakona.’+
-