Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Muzipereka kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, mʼpatseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, mʼpatseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, mʼpatseni ulemu wake.+

  • Tito 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera ndiponso kumvera maboma ndi olamulira.+ Akhalenso okonzeka kugwira ntchito iliyonse yabwino.

  • 1 Petulo 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Muzichita zimene Ambuye amafuna pogonjera ulamuliro uliwonse wokhazikitsidwa ndi anthu.+ Muzigonjera mfumu+ chifukwa ili ndi udindo waukulu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena