Mateyu 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zimene mayiyu wachita pothira mafuta onunkhirawa pathupi langa, wazichita pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+ Yohane 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Musiyeni, achite mwambo umenewu pokonzekera tsiku limene ndidzaikidwe mʼmanda.+
12 Zimene mayiyu wachita pothira mafuta onunkhirawa pathupi langa, wazichita pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+
7 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Musiyeni, achite mwambo umenewu pokonzekera tsiku limene ndidzaikidwe mʼmanda.+