Mateyu 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zimene mayiyu wachita pothira mafuta onunkhirawa pathupi langa, wazichita pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+ Maliko 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mayiyu wachita zimene akanatha. Iye wathiriratu mafuta onunkhira pathupi langa pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+ Yohane 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu nʼkuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ mogwirizana ndi mwambo umene Ayuda ankatsatira poika maliro.
12 Zimene mayiyu wachita pothira mafuta onunkhirawa pathupi langa, wazichita pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+
8 Mayiyu wachita zimene akanatha. Iye wathiriratu mafuta onunkhira pathupi langa pokonzekera kuikidwa mʼmanda kwanga.+
40 Choncho iwo anatenga mtembo wa Yesu nʼkuukulunga ndi nsalu zamaliro zonunkhira,+ mogwirizana ndi mwambo umene Ayuda ankatsatira poika maliro.