Mateyu 26:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, atamaliza kuimba nyimbo zotamanda Mulungu,* anatuluka nʼkupita kuphiri la Maolivi.+ Luka 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atachoka kumeneko anapita kuphiri la Maolivi ngati mmene ankachitira nthawi zonse ndipo ophunzira ake nawonso anamutsatira.+ Yohane 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atamaliza kunena zinthu zimenezi, Yesu anatuluka limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwoloka chigwa cha Kidironi+ kupita kumene kunali munda. Iye ndi ophunzira akewo analowa mʼmundamo.+
30 Pamapeto pake, atamaliza kuimba nyimbo zotamanda Mulungu,* anatuluka nʼkupita kuphiri la Maolivi.+
39 Atachoka kumeneko anapita kuphiri la Maolivi ngati mmene ankachitira nthawi zonse ndipo ophunzira ake nawonso anamutsatira.+
18 Atamaliza kunena zinthu zimenezi, Yesu anatuluka limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwoloka chigwa cha Kidironi+ kupita kumene kunali munda. Iye ndi ophunzira akewo analowa mʼmundamo.+