Mateyu 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako Yesu anafika nawo pamalo otchedwa Getsemane,+ ndipo anauza ophunzirawo kuti: “Khalani pansi panopa, ine ndikupita uko kukapemphera.”+ Maliko 14:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako anafika pamalo otchedwa Getsemane ndipo anauza ophunzira akewo kuti: “Khalani pansi panopa, ine ndikukapemphera.”+ Luka 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atachoka kumeneko anapita kuphiri la Maolivi ngati mmene ankachitira nthawi zonse ndipo ophunzira ake nawonso anamutsatira.+
36 Kenako Yesu anafika nawo pamalo otchedwa Getsemane,+ ndipo anauza ophunzirawo kuti: “Khalani pansi panopa, ine ndikupita uko kukapemphera.”+
32 Kenako anafika pamalo otchedwa Getsemane ndipo anauza ophunzira akewo kuti: “Khalani pansi panopa, ine ndikukapemphera.”+
39 Atachoka kumeneko anapita kuphiri la Maolivi ngati mmene ankachitira nthawi zonse ndipo ophunzira ake nawonso anamutsatira.+