Yohane 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Yesu anadziwiratu chikondwerero cha Pasika chisanafike kuti nthawi yake yochoka mʼdzikoli kupita kwa Atate+ yakwana.+ Ndipo popeza kuti ankakonda otsatira akewo amene anali mʼdzikoli, anawakonda mpaka pamapeto a moyo wake.+
13 Tsopano Yesu anadziwiratu chikondwerero cha Pasika chisanafike kuti nthawi yake yochoka mʼdzikoli kupita kwa Atate+ yakwana.+ Ndipo popeza kuti ankakonda otsatira akewo amene anali mʼdzikoli, anawakonda mpaka pamapeto a moyo wake.+